Sad
Ophunzira waku ku MUST wa final year Asimenye Mzuma wamwalira pomwe amathawa njuchi ndipo mwangozi anagwa nkuzimenyetsa pa mwala izi zachitika pamene amakwera Phiri la Midima ndi azimzake.
Mzuma analengezedwa kuti wamwalira dzulo pachipatala Cha Thyolo pomwe amalandila thandizo.
May her soul rest in peace ??
Related News
EIGHT MZUZU WARDS HAVE BEEN LEFT HOMELESS AFTER THEIR HOUSES COLLAPSED DUE TO PERSISTENT RAINFALL.
May 15, 2025
According to the report reaching our desk, Nsongwe, Saulsberry Line, Masasa, Chibavi, Zolozolo, Chip...
ABELEDWA NDALAMA MU DZINA LA CHIKONDI
May 15, 2025
Mu mau ake odyeredwa ndalama yo yemwe dzina lake ndi Mada iye wati;?
"Adha awawa ndine tinali paubw...
GABADINHO MHANGO ASUMILA TIMU YAKE ITAGWILITSA NTCHITO CHITHUNZI CHAKE MOSAENERA.